Saturday, January 18, 2025

Tag Archives: Albino Killings

FeatureNational

Simudabwa kuti kupha ma alubino kunangotha mwakachete-chete a Chakwera atatenga boma?

Ndikhulupilira kuti aMalawi tonse tikukumbukira kuti kuyambira mu chaka cha 2014 pamene a Peter Mutharika adalowa m’boma ngati mtsogoleri wadziko lino, anthu a khungu la chi alubino adasanduka nyama zakuthengo zomwe zimaphedwa ngati agwape. Zomvetsa chisoni. Moyo wa anthu achi-alubino udafika pachiwopsyezo komanso omvetsa chisoni kwambiri powasandutsa mpamba wadziwenga dzopanda chisoni. Amadulidwa ziwalo mkumakagulitsa. Ndi nkhani yomvetsa chisoni kwambiri. Pa...