Nduna yatseka Chipiku Store pa Game Complex ku LL kamba ka upandu wobisa sugar nkumanamiza anthu kuti watha
Anthu akuti ndizosangalatsa kuti President Chakwera akuyika anthu ofunikira m’malo mwawo tsopano. Anthu ochuluka anena izi pamene nduna yatsopano yowona...




















