Saturday, May 10, 2025

Tag Archives: Dr Lazaraus Chakwera

FeatureNational

WINA ASAKUNAMIZENI, INE SINDIKUCHOKA PA MPANDO WATELO PRESIDENT CHAKWERA

Lero anabwata mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazaraus Chakwera ndithudi kuyaka moto kuti buu pamene anauza khamu limene linasonkhana kumeneko kut palibe amene angamuchotse m’boma pogwiritsa ntchito mabodza. Dr Chakwera wayankhula izi lero pa mwambo otsegulira makina apamwamba a kampani ya Coca Cola Beverages Malawi Limited ku Kanengo mu mzinda wa Lilongwe, omwe azipanga zokumwa za m'maboto a pulasitiki. Mtsogoleri...