Ululu ku opposition pamene ma vendor aku Mzuzu awuza President Chakwera kuti iwo sakudana ndi Boma lake!
Anthu odziwa ndale ndi utsogoleri akamati Dr. Lazarus Chakwera awinanso, timenane izi: Taganiza, ma vendor kapena kuti ochita malonda osiyanasiyana...